Yesaya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Padzakhala msasa kuti uzipereka mthunzi woteteza ku dzuwa masana,+ ndiponso kuti ukhale pothawirapo ndi pobisalirapo mphepo yamkuntho ndi mvula.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 Yesaya 1, ptsa. 71-72
6 Padzakhala msasa kuti uzipereka mthunzi woteteza ku dzuwa masana,+ ndiponso kuti ukhale pothawirapo ndi pobisalirapo mphepo yamkuntho ndi mvula.+