Yesaya 40:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ulemerero wa Yehova ndithu udzaonekera+ ndipo anthu onse adzauonera limodzi,+ pakuti pakamwa pa Yehova m’pamene panena zimenezi.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 40:5 Yesaya 1, ptsa. 399-401 Nsanja ya Olonda,3/15/1994, tsa. 25
5 Ulemerero wa Yehova ndithu udzaonekera+ ndipo anthu onse adzauonera limodzi,+ pakuti pakamwa pa Yehova m’pamene panena zimenezi.”+