Mateyu 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Yesu analowa m’kachisi ndi kuthamangitsa onse ogulitsa ndi ogula m’kachisimo, ndipo anagubuduza matebulo a osintha ndalama ndi mabenchi a ogulitsa nkhunda.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:12 Yesu—Ndi Njira, tsa. 240 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 100 Nsanja ya Olonda,10/1/2011, tsa. 103/15/1998, tsa. 611/15/1989, tsa. 8
12 Kenako Yesu analowa m’kachisi ndi kuthamangitsa onse ogulitsa ndi ogula m’kachisimo, ndipo anagubuduza matebulo a osintha ndalama ndi mabenchi a ogulitsa nkhunda.+
21:12 Yesu—Ndi Njira, tsa. 240 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 100 Nsanja ya Olonda,10/1/2011, tsa. 103/15/1998, tsa. 611/15/1989, tsa. 8