Aroma 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiwe ndani kuti uweruze wantchito wapakhomo wa mnzako?+ Ndi udindo wa bwana wake kumuweruza kuti ndi wolakwa kapena wosalakwa.+ Komatu Yehova akhoza kumukomera mtima chifukwa angathe kumuthandiza.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:4 Nsanja ya Olonda,4/15/2010, tsa. 15
4 Ndiwe ndani kuti uweruze wantchito wapakhomo wa mnzako?+ Ndi udindo wa bwana wake kumuweruza kuti ndi wolakwa kapena wosalakwa.+ Komatu Yehova akhoza kumukomera mtima chifukwa angathe kumuthandiza.+