2 Akorinto 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ineyo ndidzagwiritsa ntchito zinthu zanga zonse ndipo ndidzadzipereka ndi moyo wanga wonse chifukwa cha miyoyo yanu.+ Ngati ineyo ndimakukondani kwambiri chonchi, kodi inuyo mukuyenera kundikonda mochepa? 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:15 Utumiki wa Ufumu,6/2007, tsa. 1 Nsanja ya Olonda,11/15/2000, tsa. 219/15/2000, ptsa. 22-23
15 Koma ineyo ndidzagwiritsa ntchito zinthu zanga zonse ndipo ndidzadzipereka ndi moyo wanga wonse chifukwa cha miyoyo yanu.+ Ngati ineyo ndimakukondani kwambiri chonchi, kodi inuyo mukuyenera kundikonda mochepa?