Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlungu Uno
October 27–November 2
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—2025 | September

OCTOBER 27–NOVEMBER 2

MLALIKI 11-12

Nyimbo Na. 155 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Muzikhala Athanzi Komanso Osangalala

(10 min.)

Ngati n’zotheka muzipeza nthawi kuti muziwombedwako dzuwa komanso kupitidwako kamphepo (Mla 11:7, 8; g 3/15 13 ¶6-7)

Muzisamalira thanzi lanu komanso muzisamala ndi zimene mumaganiza (Mla 11:10; w23.02 21 ¶6-7)

Koposa zonse, muzilambira Yehova ndi mtima wonse (Mla 12:13; w24.09 2 ¶2-3)

Banja lachikulire likusamalira maluwa mosangalala.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Mla 12:9, 10—Kodi mavesiwa akutiphunzitsa chiyani zokhudza amuna amene Mulungu anawagwiritsa ntchito kuti alembe Baibulo? (it “Kuuzira” ¶10)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Mla 12:1-14 (th phunziro 12)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Wobwereza

(3 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. (lmd phunziro 8 mfundo 3)

5. Ulendo Wobwereza

(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Pa ulendo wapita, mwininyumbayo anakuuzani kuti wachibale wake kapena mnzake wamwalira. (lmd phunziro 9 mfundo 3)

6. Nkhani

(5 min.) lmd zakumapeto A mfundo 13—Mutu: Mulungu Amafuna Kutithandiza. (th phunziro 20)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 111

7. Zofunika Pampingo

(15 min.)

8. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) lfb mutu 30-31

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 8 ndi Pemphero

Zimene Zili M’magaziniyi
Nsanja ya Olonda (Yophunzira)—2025 | August

Nkhani Yophunzira 34: October 27, 2025–November 2, 2025

14 Musamakayikire Kuti Yehova Amakhululuka

Nkhani Zina

Nkhani zina za m'magaziniyi

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena