1
Moni (1-3)
Paulo ayamika Mulungu cifukwa ca Akhristu a ku Korinto (4-9)
Awalimbikitsa kukhala ogwilizana (10-17)
Khristu ndi mphamvu komanso nzelu ya Mulungu (18-25)
Kudzitama mwa Yehova (26-31)
2
Ulaliki wa Paulo ku Korinto (1-5)
Nzelu za Mulungu n’zapamwamba kwambili (6-10)
Kusiyana kwa munthu wauzimu ndi munthu wokonda zinthu za m’dziko (11-16)
3
Akorinto akucitabe zinthu ngati anthu akuthupi (1-4)
Mulungu ndiye amakulitsa (5-9)
Kumanga ndi zinthu zosagwila moto (10-15)
Ndinu kacisi wa Mulungu (16, 17)
Nzelu za m’dzikoli n’zopusa kwa Mulungu (18-23)
4
Atumiki ayenela kukhala okhulupilika (1-5)
Atumiki a Cikhristu ayenela kukhala odzicepetsa (6-13)
Paulo asamalila ana ake akuuzimu (14-21)
5
Nkhani ya munthu amene anacita ciwelewele (1-5)
Yisiti wocepa amafufumitsa mtanda wonse (6-8)
Munthu woipa ayenela kucotsedwa (9-13)
6
Akhristu kutengelana ku makhoti (1-8)
Amene sadzalowa mu Ufumu wa Mulungu (9-11)
Lemekezani Mulungu ndi matupi anu (12-20)
7
Malangizo kwa anthu osakwatila komanso kwa okwatila (1-16)
Mukhalebe mmene munalili pamene Mulungu anakuitanani (17-24)
Anthu osakwatila komanso akazi amasiye (25-40)
8
9
10
Zitsanzo zoticenjeza zokhudza mbili ya Aisiraeli (1-13)
Cenjezo pa nkhani ya kulambila mafano (14-22)
Ufulu komanso kuganizila ena (23-33)
11
“Tengelani citsanzo canga” (1)
Umutu komanso kubvala cophimba kumutu (2-16)
Kucita mwambo wa Mgonelo wa Ambuye (17-34)
12
13
14
15
Kuuka kwa Khristu (1-11)
Kuuka kwa akufa ndiwo maziko a cikhulupililo (12-19)
Kuuka kwa Khristu kutitsimikizila kuti akufa adzauka (20-34)
Thupi la mnofu, thupi lauzimu (35-49)
Thupi limene silingafe komanso kuola (50-57)
Zocita zambili mu nchito ya Ambuye (58)
16
Kusonkhanitsa zopeleka za Akhristu a ku Yerusalemu (1-4)
Maulendo amene Paulo anali kufuna kuyenda (5-9)
Akonza za ulendo wa Timoteyo komanso Apolo (10-12)
Malangizo komanso kupeleka moni (13-24)