AGALATIYA
ZA M’BUKULI
-
Nchito za Cilamulo komanso cikhulupililo (1-14)
Wolungama adzakhala ndi moyo cifukwa ca cikhulupililo (11)
Lonjezo la Abulahamu silidalila Cilamulo (15-18)
Khristu, mbadwa ya Abulahamu (16)
Ciyambi ca Cilamulo komanso colinga cake (19-25)
Ana a Mulungu cifukwa ca cikhulupililo (26-29)
Ake a Khristu ndi mbadwa za Abulahamu (29)