Zamkati
Peji
4 Kodi Tingamumvetsele Bwanji Mulungu?
8 Kodi Umoyo Unali Bwanji m’Paladaiso?
10 Anamvetsela kwa Satana—Nanga Cinacitika n’Ciani?
12 Cigumula ca Nowa—Ndani Anamvetsela? Ndani Sanamvetsele?
14 Kodi Cigumula ca Nowa Cimatiphunzitsa Ciani?
18 Kodi Timapindula Bwanji ndi Imfa ya Yesu?
20 Kodi Paladaiso Idzabwela Liti?
22 Kodi Amene Amamvetsela kwa Mulungu Adzapeza Madalitso Abwanji?
24 Kodi Yehova Amamvetsela kwa Ife?
26 Mungacite Ciani Kuti Banja Likhale Lokondweletsa?
28 Kodi Tiyenela Kucita Ciani Kuti Tikondweletse Mulungu?
30 Kodi Mungaonetse Bwanji Kuti Ndinu Okhulupilika kwa Yehova?