Zamkati
October 15, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
YOPHUNZILA
DECEMBER 1-7, 2014
Khalani ndi Cikhulupililo Cosagwedela mu Ufumu
TSAMBA 7 • NYIMBO: 108, 129
DECEMBER 8-14, 2014
TSAMBA 13 • NYIMBO: 98, 102
DECEMBER 15-21, 2014
Muziyamikila Mwai Wanu Wogwila Nchito ndi Yehova
TSAMBA 23 • NYIMBO: 120, 44
DECEMBER 22-28, 2014
“Ikani Maganizo Anu pa Zinthu Zakumwamba”
TSAMBA 28 • NYIMBO: 70, 57
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ Khalani ndi Cikhulupililo Cosagwedela mu Ufumu
▪ Mudzakhala “Ufumu wa Ansembe”
Ufumu wa Mesiya ndiwo njila yokha imene Yehova adzagwilitsila nchito kuti akwanilitse cifunilo cake ca dziko lapansi ndi ca anthu. Pamene tikambilana mapangano angapo ochulidwa m’Baibulo, tidzaphunzila mmene amagwilizanilana ndi boma lakumwamba. Tidzaphunzila cifukwa cake tiyenela kukhala ndi cidalilo colimba mu Ufumu.
▪ Muziyamikila Mwai Wanu Wogwila Nchito ndi Yehova
M’nkhani ino, tidzaphunzila zitsanzo zakale ndi zamakono za anthu amene atumikila Yehova. Idzatithandiza kuyamikila mwai wathu wogwila nchito ndi Mulungu, umene tiyenela kuyamikila kwambili.
▪ “Ikani Maganizo Anu pa Zinthu Zakumwamba”
M’masiku ano otsiliza, timakumana ndi zinthu zambili zimene zimayesa cikhulupililo cathu. Nanga tingaphunzile ciani kwa anthu akale monga Abulahamu ndi Mose, amene anakumana ndi mayeselo ofanana ndi athu? Nkhani ino idzatithandiza kupilila ndi kutilimbikitsa kuika maganizo athu pa Mulungu ndi Ufumu wake.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
CIKUTO: Alongo aŵili alalikila kwa anthu amene akuyenda mumseu waukulu pafupi ndi mapili a Mbololo, kum’mawa koma cakum’mwela pang’ono m’tauni ya Tausa, ku Taita
KU KENYA
KULI ANTHU
44,250,000
OFALITSA
26,060
MAPHUNZILO A BAIBULO
43,034
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO MU 2013
60,166