Ndandanda ya Mlungu wa August 26
MLUNGU WA AUGUST 26
Nyimbo 63 ndi Pemphelo
□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:
bt mutu 28 ndime 1 mpaka 7 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibo: Aroma 13 mpaka 16 (Mph. 10)
Kubweleza za M’sukulu ya Ulaliki (Mph. 20)
□ Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 11
Mph. 10: “Limbikitsani Kuyambitsa Maphunzilo a Baibo pa Ciŵelu Coyamba.” Nkhani. Pambuyo pake, mucite citsanzo ca mmene mungayambitsile phunzilo la Baibo pa Ciŵelu coyamba mu September. Limbikitsani onse kutengamo mbali.
Mph. 10: Njila Zolalikilila Uthenga Wabwino—Gawo la Mpingo Komanso Gawo Lanu-lanu. Nkhani yokambilana yocokela m’buku la Gulu, patsamba 102, ndime 3 mpaka tsamba 104, ndime 1. Funsani mafunso mtumiki wa magawo za makonzedwe a mpingo wanu okhalila ndi gawo logwililamo nchito.
Mph. 10: Cifukwa Cake Sindife Aneneli Onama. Nkhani yokambilana yocokela m’buku la Kukambitsilana, patsamba 35, ndime 3 mpaka kumapeto kwa tsamba 36.
Nyimbo 116 ndi Pemphelo