Ndandanda ya Mlungu wa June 29
MLUNGU WA JUNE 29
Nyimbo 9 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 11 ndime 17-22 ndi bokosi pa tsa. 116 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: 1 Mafumu 3-6 (Mph. 8)
Kubweleza za m’Sukulu ya Ulaliki (Mph. 20)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: “Kumbukilani masiku akale.”—Deut. 32:7.
Nyimbo 118
Mph. 15: Zogaŵila mu July. Kukambilana. Kambilanani nkhani zimene zili mu zofalitsa zimene tidzagaŵila, ndipo mucite citsanzo coonetsa ofalitsa akuphunzitsa watsopano kugaŵila cofalitsa.
Mph. 15: Kalata Yocokela ku Bungwe Lolamulila. Kukambilana. Pemphani omvela kufotokoza mbali zolimbikitsa za lipoti la padziko lonse ndi za m’dziko lathu mu caka cautumiki capita.
Nyimbo 108 ndi Pemphelo