LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 April tsa. 4
  • April 16-22

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 16-22
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 April tsa. 4

April 16-22

MALIKO 1-2

  • Nyimbo 130 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Macimo Ako Akhululukidwa”: (10 min.)

    • [Tambani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Maliko.]

    • Maliko 2:3-5—Yesu mwacifundo anakhululukila macimo munthu wakufa ziwalo (jy peji 67 mapa. 3-5)

    • Maliko 2:6-12—Yesu anaonetsa kuti ali na mphamvu zokhululukila macimo mwa kucilitsa munthu wakufa ziwalo (“Capafupi n’citi” nwtsty mfundo younikila pa Maliko 2:9)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Maliko 1:11—Kodi mau amene Yehova anauza Yesu atanthauza ciani? (“panamveka mau ocokela kumwamba,” “ndiwe Mwana wanga,” “ndimakondwela nawe” nwtsty mfundo zounikila)

    • Maliko 2:27, 28—N’cifukwa ciani Yesu anadzicha kuti “Mbuye wa sabata”? (“Mbuye . . . wa sabata” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Maliko 1:1-15

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. Olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Yankhani pa zimene anthu a m’gawo lanu amakamba posafuna kulalikidwa.

  • Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano a citsanzo.

  • Vidiyo ya Kubwelelako Kaciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 44

  • “Sindinabwele Kudzaitana Anthu Olungama, Koma Ocimwa”: (7 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti N’tacoka m’Ndende n’Nakhala na Umoyo Wabwino Ndiyeno, funsani mafunso otsatilawa: N’ciani cinathandiza Donald kupeza cimwemwe ceni-ceni? Pophunzitsa, tingatengele bwanji khalidwe la Yesu lopanda tsankho pocita zinthu na anthu?—Maliko 2:17.

  • Yehova Amakhululuka “ndi Mtima Wonse”: (8 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Yehova, Muzakhala pa Malo Oyamba. Ndiyeno, funsani mafunso aya: N’cifukwa ciani Anneliese anabwelela kwa Yehova? Nanga anacita ciani kuti abwelele? (Yes. 55:6, 7) Kodi cocitika cake mungaciseŵenzetse bwanji pothandiza anthu amene anasiya Yehova?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 17

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 86 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani