CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MALIKO 1-2
“Macimo Ako Akhululukidwa”
Tiphunzilapo ciani pa cozizwitsa ici?
Kudwala kunabwela kaamba ka ucimo
Yesu ali na mphamvu zokhululukila macimo na kucilitsa odwala
Mu Ufumu wa Mulungu, Yesu adzacotsa ucimo na matenda kwamuyaya
Kodi lemba la Maliko 2:5-12 linganithandize bwanji kupilila nikadwala?