Mau oyamba
MUGANIZA BWANJI?
Kodi wopambana onse pa kupeleka mphatso n’ndani?
“Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwilo imacokela kumwamba, pakuti imatsika kucokela kwa Atate wa zounikila zonse zakuthambo, ndipo iye sasintha ngati kusuntha kwa mthunzi.”—Yakobo 1:17.
Magaziniyi ya Nsanja ya Mlonda idzatithandiza kudziŵa mphatso imodzi yoposa zonse, yocokela kwa Mulungu.