LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 June tsa. 6
  • “Mulungu Ndiye Mthandizi Wanga”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Mulungu Ndiye Mthandizi Wanga”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • “Umutulile Yehova Nkhawa Zako”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Yehova Amathandiza Odwala
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Khalani Wodzicepetsa Ena Akakutamandani
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 June tsa. 6

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

“Mulungu Ndiye Mthandizi Wanga”

Masalimo 52-59 aonetsa zokamba za Davide panthawi imene anali kukumana ndi mavuto. Komabe, iye anadalilabe Yehova panthawi zovuta zimenezo. (Sal. 54:4; 55:22) Anatamanda Yehova cifukwa ca mau Ake. (Sal. 56:10) Kodi nafenso timakhulupilila ndi kudalila Mulungu monga Davide? Kodi timalola Mau ake kutitsogolela tikakumana ndi mavuto? (Miy. 2:6) Ni mavesi ati a m’Baibulo amene anakuthandiza pamene munali . . .

  • kuvutika maganizo?

  • kudwala?

  • wokhumudwa ndi zocita za ena?

  • kuzunzidwa?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani