LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 October tsa. 1
  • Maulaliki a Citsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki a Citsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • GALAMUKANI!
  • PHUNZITSANI COONADI
  • KODI N’ZOONA KUTI AKUFA ANGAKHALENSO NDI MOYO? (T-35)
  • KONZANI ULALIKI WANU
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 October tsa. 1
M’bale agaŵila kapepa kauthenga kakuti Akufa Angakhalenso Ndi Moyo m’Cituvalu

Agaŵila kapepa kauthenga kakuti Akufa Angakhalenso Ndi Moyo m’Cituvalu

Maulaliki a Citsanzo

GALAMUKANI!

Galamukani! Na. 5 2017 | Zimene Tingachite Kuti Tipulumuke Pakachitika Ngozi Zadzidzidzi

Funso: N’cifukwa ciani tifunika kukonzekela masoka a zacilengedwe?

Lemba: Miy. 27:12

Cogaŵila: Galamukani! iyi ifotokoza zimene tingacite masoka akalibe kucitika, panthawi ya masoka, na pambuyo pake?

PHUNZITSANI COONADI

Baibo yotsegula

Funso: Kodi tingaonetse bwanji kuti timam’konda Mulungu?

Lemba: 1 Yoh. 5:3

Coonadi: Timaonetsa cikondi cathu kwa Mulungu mwa kumvela malamulo ake.

KODI N’ZOONA KUTI AKUFA ANGAKHALENSO NDI MOYO? (T-35)

Kodi N’zoona Kuti Akufa Angakhalenso Ndi Moyo?

Funso: Anthu ambili oona mtima padziko lapansi amacita miyambo yokumbukila akufa. Kodi pali ciyembekezo cakuti tidzaonananso na okondedwa athu amene anamwalila?

Lemba: Mac. 24:15

Cogaŵila: Kapepa kauthenga aka kafotokoza mapindu okhulupilila kuti akufa adzauka. [Ngati n’kotheka, m’tambitseni kavidiyo kakuti Kodi Pali Ciyembekezo Cakuti Akufa Adzauka?]

KONZANI ULALIKI WANU

Funso:

Lemba:

Cogaŵila:

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani