LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 July tsa. 4
  • Wosamvela Malamulo Aonekela

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Wosamvela Malamulo Aonekela
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Nkhani Zofanana
  • “Khalanibe Maso”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 July tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 2 2 ATESALONIKA 1-3

Wosamvela Malamulo Aonekela

2:6-12

Kodi Paulo anali kutanthauza ciani pa mavesiwa?

  • Akhristu a mpatuko asokoneza msonkhano wa Akhristu a mu mpingo woyambilila

    ‘Cocititsa’ (vs. 6)—Mwacionekele ni atumwi

  • ‘Kuonekela’ (vs. 6)—Atumwi atamwalila, Akhristu a mpatuko anaonekela poyela n’kuyamba kuphunzitsa zinthu zabodza na kucita zinthu mwacinyengo

  • “Cinsinsi ca kusamvela malamulo” (vs. 7)—“Wosamvela malamulo” sanadziŵike bwino-bwino m’nthawi ya Paulo

  • Gulu la atsogoleli a Machalichi Acikhristu likalipila m’bale amene wanyamula Baibo m’manja.

    “Wosamvela malamulo” (vs. 8)—Masiku ano ni atsogoleli onse a machalichi acikhristu

  • “Ambuye Yesu adzamuthetsa [wosamvela malamulo]. . . pa nthawi imene kukhalapo kwa Yesuyo kudzaonekele “ (vs. 8)—Yesu adzaonetsa poyela kuti ni Mfumu akadzapeleka ciweluzo ca Yehova pa dongosolo lino la Satana, komanso kwa “wosamvela malamulo”

Kodi mavesiwa akulimbikitsani bwanji pa nkhani ya kulalikila mwakhama ndiponso mwacangu?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani