CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 YOHANE 1-5
Musamakonde Dziko Kapena Zinthu za M’dziko
2:15-17
Satana amaseŵenzetsa zinthu zitatu zotsatilazi, zimene ni zokopa za dzikoli, pofuna kuticotsa kwa Yehova. Kodi zinthu zimenezi mungazifotokoze bwanji kwa munthu wina?
“Cilakolako ca thupi”
“Cilakolako ca maso”
“Kudzionetsela ndi zimene munthu ali nazo pa moyo wake”