LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsa. 8
  • Na Thandizo la Yehova, Mungakwanitse Kucita Utumiki Wovuta

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Na Thandizo la Yehova, Mungakwanitse Kucita Utumiki Wovuta
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Tate Apeleka Uphungu Wacikondi kwa Mwana Wake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Khalanibe na Mantha Oyenela Oopa Kukhumudwitsa Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Thandizani Acinyamata Kuti Apambane
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Kulambila pa Kacisi Kunayamba Kucitika Mwadongosolo Kwambili
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 January tsa. 8

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Na Thandizo la Yehova, Mungakwanitse Kucita Utumiki Wovuta

Alevi olondela zipata anali na udindo waukulu (1 Mbiri 9:26, 27; w05 10/1 9 ¶8)

Pinihasi ndiye anali kuyang’anila alonda a pa zipata za pa cihema m’nthawi ya Mose (1 Mbiri. 9:17-20a)

Yehova anamuthandiza Pinihasi kukwanilitsa utumiki wake (1 Mbiri 9:20b; w11 9/15 32 ¶7)

Zithunzi: 1. Mlongo wacitsikana akuyendetsa cigalimoto coseŵenzetsa pa nchito yomanga. 2. M’bale wacikulile na mkazi wake akucita ulaliki wa pafoni. 3. M’bale na mkazi wake akulalikila m’dela losoŵa.

Yehova amatipatsa nchito zambili zofunika. Ngati simudziŵa mocitila utumiki umene mwapatsidwa, pemphelani kwa Yehova na kufunsila kwa Mkhristu wokhwima mwauzimu kuti akuthandizeni.—Afil. 2:13.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani