LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 2
  • “Musalowelele Nchito Yomanga Nyumba ya Mulungu”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Musalowelele Nchito Yomanga Nyumba ya Mulungu”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Mukukumbukila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2022
  • Lolani Kuti Yehova Akugwilitseni Nchito
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Musawasiye Konse Alambili Anzanu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Ni Nthawi Iti Pamene Tiyenela Kudalila Yehova?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 2

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Musalowelele Nchito Yomanga Nyumba ya Mulungu”

Mkulu wa Ansembe Yesuwa (Yoswa) na Bwanamkubwa Zerubabele anatsogolela pa nchito yomanganso kacisi, ngakhale kuti nchitoyo inali yoletsedwa (Ezara 5:1, 2; w22.03 18 ¶13)

Pamene otsutsa anafunsa Ayuda kuti ndani anawavomeleza kumanga, iwo anafotokoza za lamulo la Koresi (Ezara 5:3, 17; w86 2/1 29, bokosi ¶2-3)

Mfumuyo inatsimikizila za lamulo loyamba lija, ndiponso inalamula otsutsawo kuti aleke kuloŵelela pa nchito yomangayo (Ezara 6:7, 8; w22.03 15 ¶7)

Mlongo akutamba pulogilamu ya JW Broadcasting ndipo m’maganizo mwake akuyelekezela kuti akuona Zerubabele na Mkulu wa Ansembe Yesuwa akutsogolela Aisreali panchito yomanganso kacisi.

ZOYENELA KUSINKHASINKHA: Kodi nkhani ya m’Baibo imeneyi itilimbikitsa bwanji kutsatila malangizo a anthu oikidwa na Yehova kuti azititsogolela, ngakhale kuti malangizowo sitikuwamvetsa?—w22.03 19 ¶16.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani