LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 14
  • Lolani Kuti Yehova Akugwilitseni Nchito

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Lolani Kuti Yehova Akugwilitseni Nchito
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • “Musalowelele Nchito Yomanga Nyumba ya Mulungu”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Kodi Mukukumbukila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2022
  • Zotulukapo Zowawa za Kusamvela
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Khalidwe la Ezara Linacititsa Kuti Yehova Alemekezeke
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 14

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Lolani Kuti Yehova Akugwilitseni Nchito

[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Ezara.]

Yehova analimbikitsa mtima wa Mfumu Koresi kuti amasule Aisiraeli mu ukapolo (Ezara 1:1-3; w22.03 14 ¶1)

Yehova analimbikitsa mitima ya anthu ake kuti akamangenso kacisi (Ezara 1:5; w17.10 26 ¶2)

M’bale akugwilitsa nchito Baibo potonthoza m’bale wina na mkazi wake amene ali m’cipatala cifukwa covulala kwambili.

Ngati ndinu wodzipeleka, Yehova angakupangitseni kukhala ciliconse cimene afuna kuti akwanilitse cifunilo cake.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani