LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 5
  • Zotulukapo Zowawa za Kusamvela

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zotulukapo Zowawa za Kusamvela
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Kutumikila Yehova Sikovuta
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • “Kodi Yehova Mulungu Wanu Akufuna Kuti Muzicita Ciani?”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Lolani Kuti Yehova Akugwilitseni Nchito
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Baibo—Buku Limene Limakamba Zenizeni Osati Nthano
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 5

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zotulukapo Zowawa za Kusamvela

Aisiraeli ena anapanga mgwilizano wa ukwati na anthu olambila mafano (Ezara 9:1, 2; w06 1/15 20 ¶1)

Iwo ananyalanyaza malamulo omveka bwino a Yehova (Ezara 9:10-12)

Kusamvela kwawo kunabweletsa mavuto aakulu pa iwo na mabanja awo (Ezara 10:10, 11, 44)

Mlongo amene anakwatiwa na munthu amene si Mboni, tsopano ali na mwana, ndipo akuyewa mmene umoyo wake unalili pamene anali wacangu kuuzimu. Patebulo pali koikapo ndudu. Mwamuna wake amene wakhuta mowa ali gone pa sofa.

Lamulo lililonse la Yehova limatipindulila. (w09 10/1 10 ¶6) Kumvela kudzatiteteza ku mavuto pali pano, komanso kudzathandiza kuti tikalandile madalitso osatha kutsogolo.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi kumvela Yehova kwaniteteza bwanji ku mavuto?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani