LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsa. 4
  • Baibo—Buku Limene Limakamba Zenizeni Osati Nthano

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Baibo—Buku Limene Limakamba Zenizeni Osati Nthano
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Kutumikila Yehova Sikovuta
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • “Kodi Yehova Mulungu Wanu Akufuna Kuti Muzicita Ciani?”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Yehova Amadalitsa Anthu Ocita Zinthu Molimba Mtima
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Mmene Mungakhalile Bwenzi Labwino
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 January tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Baibo—Buku Limene Limakamba Zenizeni Osati Nthano

[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 1 Mbiri.]

Adamu anali munthu weniweni (1 Mbiri 1:1;w09 9/1 14 ¶1)

Nowa nayenso anali munthu weniweni (1 Mbiri 1:4; w08 6/1 3 ¶4)

M’bale akusinkha-sinkha zimene akuŵelenga m’Baibo. M’maganizo mwake akuona Nowa na banja lake akumanga cingalawa.

Tikadziŵa kuti anthu ochulidwa m’Baibo sanali ongopeka, timapindula kwambili na zitsanzo zawo.—1 Akor. 15:22; w09 9/1 14-15.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani