LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsa. 13
  • Muzim’kumbukila Yehova Nthawi Zonse

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Muzim’kumbukila Yehova Nthawi Zonse
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Jason Worilds: Ukamatumikila Yehova Umangopambana Basi
    Baibo Imasintha Anthu
  • Kodi Yehova Aiona Bwanji Nkhaniyi?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Sangalalani Cifukwa Cogwila Nchito Yanu Mwakhama
    “Khalanibe m’Cikondi ca Mulungu”
  • Mmene Tingapangile Zisankho Zabwino
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 September tsa. 13

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Muzim’kumbukila Yehova Nthawi Zonse

Ngati zikutivuta kupeza nchito yakuthupi, cingakhale covuta kupitiliza kuika Ufumu wa Mulungu patsogolo mu umoyo wathu na cilungamo cake. Tingakhale pa mayeselo ovomela kugwila nchito imene ingasokoneze utumiki wathu kwa Yehova, kapena imene imasemphana na mfundo za m’Baibo. Komabe, tiyenela kukhala otsimikiza kuti Yehova amaonetsa mphamvu zake “kwa anthu amene mtima wawo uli wathunthu kwa iye.” (2 Mbiri 16:9) Kulibe cimene cingalepheletse Atate wathu wacikondi kutithandiza na kutipatsa zimene timafunikila. (Aroma 8:32) Conco, pamene tipanga zisankho zokhudza nchito, tiyenela kudalila Yehova na kusumika maganizo athu pa kum’tumikila.—Sal. 16:8.

ONELELANI VIDIYO YAKUTI TUMIKILANI YEHOVA NA MOYO WANU WONSE, NDIYENO YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • Cithunzi coonetsa zocitika za mu vidiyo yakuti “Tumikilani Yehova na Moyo Wanu Wonse.” Thomas akuona pamene Jason akukana kulandila ciphuphu ku nchito.

    N’cifukwa ciani m’bale Jason anakana kulandila ciphuphu?

  • Cithunzi coonetsa zocitika za mu vidiyo yakuti “Tumikilani Yehova na Moyo Wanu Wonse.” Jason akutenga zinyalala ku nchito n’kukazitaya.

    Kodi Akolose 3:23 tingaiseŵenzetse bwanji?

  • Cithunzi coonetsa zocitika za mu vidiyo yakuti “Tumikilani Yehova na Moyo Wanu Wonse.” Jason akum’phunzitsa Baibo Thomas.

    Kodi citsanzo cabwino ca m’bale Jason cinam’khudza bwanji Thomas?

  • Cithunzi coonetsa zocitika za mu vidiyo yakuti “Tumikilani Yehova na Moyo Wanu Wonse.” Jason na Thomas akomboka ku nchito nthawi ikaliko kuti akapezeke kumisonkhano.

    Lolani Yehova kukutsogolelani pa zisankho zanu na zocita zanu

    Kodi Mateyu 6:22 tingaiseŵenzetse bwanji?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani