LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 88
  • N’dziŵitseni Njila Zanu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • N’dziŵitseni Njila Zanu
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Ndidziwitseni Njira Zanu
    Imbirani Yehova
  • Khulupilila Coonadi Iwe Mwini
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Inuyo Panokha Muzikonda Kwambiri Choonadi
    Imbirani Yehova
  • Mvelani Pemphelo Langa Conde
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 88

NYIMBO 88

N’dziŵitseni Njila Zanu

Yopulinta

(Salimo 25:4)

  1. 1. Tasonkhana pano Yehova M’lungu,

    Inu ndinu mwatiitana.

    Mu mau anu ise timapeza

    Maphunzilo aumulungu.

    (KOLASI)

    O Yehova, ine phunzitseni,

    Nifuna nidziŵe njila zanu.

    N’thandizeni kuti nthawi zonse

    Niziyenda m’njila ya co’nadi.

  2. 2. Nzelu zanu Yehova n’zodabwitsa,

    Ise zimatilimbikitsa.

    Timapindula na co’nadi canu

    Copatsa moyo wamuyaya.

    (KOLASI)

    O Yehova, ine phunzitseni,

    Nifuna nidziŵe njila zanu.

    N’thandizeni kuti nthawi zonse

    Niziyenda m’njila ya co’nadi.

(Onaninso Eks. 33:13; Sal. 1:2; 119:27, 35, 73, 105.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani