Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ezara 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iwo anayamba kuimba+ potamanda ndi kuyamika Yehova kuti, “iye ndi wabwino, chikondi chokhulupirika chimene amachisonyeza kwa Isiraeli chidzakhalapo mpaka kalekale.”+ Kenako anthu onse anafuula kwambiri potamanda Yehova chifukwa cha kumangidwa kwa maziko a nyumba ya Yehova.

  • Salimo 106:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Tipulumutseni inu Yehova Mulungu wathu,+

      Ndi kutisonkhanitsa pamodzi kuchokera mʼmitundu ina,+

      Kuti titamande dzina lanu loyera,

      Komanso kuti tikutamandeni mosangalala.+

  • Yesaya 49:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Fuulani mosangalala kumwamba inu ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+

      Mapiri asangalale ndipo afuule mosangalala.+

      Chifukwa Yehova watonthoza anthu ake+

      Ndipo wachitira chifundo anthu ake ovutika.+

  • Yeremiya 31:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iwo adzabwera nʼkufuula mosangalala pamwamba pa phiri la Ziyoni.+

      Nkhope zawo zidzawala chifukwa cha ubwino wa* Yehova.

      Chifukwa cha mbewu, vinyo watsopano+ ndi mafuta,

      Ndiponso chifukwa cha ana a nkhosa ndi ana a ngʼombe.+

      Iwo adzakhala ngati dimba lothiriridwa bwino+

      Ndipo sadzakhalanso ofooka.”+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani