-
Yeremiya 25:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Choncho Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘“Chifukwa simunamvere mawu anga,
-
-
Yeremiya 25:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Dziko lonseli lidzakhala bwinja ndipo lidzakhala chinthu chochititsa mantha. Mitundu imeneyi idzatumikira mfumu ya ku Babulo zaka 70.”’+
-
-
Yeremiya 27:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Tsopano ndapereka mayiko onsewa mʼmanja mwa mtumiki wanga, Mfumu Nebukadinezara+ ya ku Babulo. Ndamupatsanso ngakhale nyama zakutchire kuti zimutumikire.
-