2 Akorinto 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Takhala tikulankhula mosabisa mawu kwa inu Akorinto, tafutukula mtima wathu.+ 2 Akorinto 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Sikuti ndanena izi kuti ndikutsutseni ngati olakwa ayi. Pajatu ndanena kale kuti inuyo muli m’mitima yathu, kaya tife kapena tikhale moyo.+ 2 Akorinto 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ineyo ndidzagwiritsa ntchito zinthu zanga zonse ndipo ndidzadzipereka ndi moyo wanga wonse chifukwa cha miyoyo yanu.+ Ngati ineyo ndimakukondani kwambiri chonchi, kodi inuyo mukuyenera kundikonda mochepa?
3 Sikuti ndanena izi kuti ndikutsutseni ngati olakwa ayi. Pajatu ndanena kale kuti inuyo muli m’mitima yathu, kaya tife kapena tikhale moyo.+
15 Koma ineyo ndidzagwiritsa ntchito zinthu zanga zonse ndipo ndidzadzipereka ndi moyo wanga wonse chifukwa cha miyoyo yanu.+ Ngati ineyo ndimakukondani kwambiri chonchi, kodi inuyo mukuyenera kundikonda mochepa?