Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 34:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Zipatso zoyamba kucha zabwino koposa+ za m’munda mwanu muzibwera nazo kunyumba ya Yehova Mulungu wanu.+

      “Musawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi wake.”+

  • Numeri 18:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Ndakupatsa iwe zipatso zoyambirira+ za mafuta onse abwino koposa, vinyo yense watsopano wabwino koposa, ndi mbewu zabwino koposa, zimene anthu azizipereka kwa Yehova.+

  • Nehemiya 10:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Tinachita maerewo kuti tipezenso wobweretsa kunyumba ya Yehova zipatso zoyamba kucha m’dziko lathu+ chaka ndi chaka, ndi zipatso zoyamba kucha mwa zipatso zonse za mtengo uliwonse.+

  • 1 Akorinto 15:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Komabe, Khristu anaukitsidwa kwa akufa,+ n’kukhala chipatso choyambirira+ cha amene akugona mu imfa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena