Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 36:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako anapanga ngowe 50 zagolide ndi kulumikiza nsalu ndi ngowezo kuti nsaluzo zikhale chinsalu chimodzi cha chihema.+

  • Ekisodo 39:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Pamenepo anabweretsa kwa Mose chihema chopatulika+ ndi zipangizo zake zonse,+ nsalu yake yophimba pamwamba,+ ngowe zake,+ mafelemu ake,+ mitengo yake yonyamulira,+ mizati yake ndi zitsulo zamphako zoika pansi.+

  • Aheberi 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chihema chimenecho chinali chifaniziro+ cha nthawi yoikidwiratu imene tsopano yafika,+ ndipo mogwirizana ndi chifanizirocho, zonse ziwiri, mphatso ndi nsembe zimaperekedwa.+ Komabe, zimenezi sizipangitsa munthu amene akuchita utumiki wopatulikayo kukhala wangwiro+ m’chikumbumtima chake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena