Ekisodo 40:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno udzaike guwa lansembe lagolide la zofukiza,+ patsogolo pa likasa la umboni, ndi kuika nsalu yotchinga pakhomo la chihema chopatulika.+ Salimo 141:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pemphero langa likhale lokonzedwa ngati zofukiza+ pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+
5 Ndiyeno udzaike guwa lansembe lagolide la zofukiza,+ patsogolo pa likasa la umboni, ndi kuika nsalu yotchinga pakhomo la chihema chopatulika.+
2 Pemphero langa likhale lokonzedwa ngati zofukiza+ pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+