Ekisodo 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe Farao sadzakumverani,+ motero ndidzaonetsa mphamvu ya dzanja langa pa Iguputo ndi kutulutsa makamu anga,+ anthu anga,+ ana a Isiraeli,+ m’dziko la Iguputo ndi ziweruzo zamphamvu.+ Ekisodo 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Mawa ukalawirire m’mawa kwambiri kukaonana ndi Farao,+ ndipo ukamuuze kuti: ‘Yehova Mulungu wa Aheberi wanena kuti: “Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.+
4 Komabe Farao sadzakumverani,+ motero ndidzaonetsa mphamvu ya dzanja langa pa Iguputo ndi kutulutsa makamu anga,+ anthu anga,+ ana a Isiraeli,+ m’dziko la Iguputo ndi ziweruzo zamphamvu.+
13 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Mawa ukalawirire m’mawa kwambiri kukaonana ndi Farao,+ ndipo ukamuuze kuti: ‘Yehova Mulungu wa Aheberi wanena kuti: “Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.+