Ekisodo 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’mawa upite kwa Farao. Iyetu adzakhala akupita kumtsinje.+ Choncho iweyo ukaime poti ukathe kukumana naye m’mphepete mwa mtsinje wa Nailo,+ ndipo udzatenge ndodo imene inasanduka njoka ija.+
15 M’mawa upite kwa Farao. Iyetu adzakhala akupita kumtsinje.+ Choncho iweyo ukaime poti ukathe kukumana naye m’mphepete mwa mtsinje wa Nailo,+ ndipo udzatenge ndodo imene inasanduka njoka ija.+