Ekisodo 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Mawa ukalawirire m’mawa kwambiri kukaonana ndi Farao,+ ndipo ukamuuze kuti: ‘Yehova Mulungu wa Aheberi wanena kuti: “Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.+
13 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Mawa ukalawirire m’mawa kwambiri kukaonana ndi Farao,+ ndipo ukamuuze kuti: ‘Yehova Mulungu wa Aheberi wanena kuti: “Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.+