Ekisodo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzatambasula dzanja langa ndi kukantha Iguputo.+ Motero ndidzatulutsa ana a Isiraeli m’dzikolo.”+ Ekisodo 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa tsiku limenelo ndidzapatula dera la Goseni kumene kuli anthu anga, kuti kusakhale tizilombo toyamwa magazi.+ Ndidzatero kuti udziwe kuti ine ndine Yehova, ndipo ndili ndi mphamvu padziko lonse lapansi.+ Ezekieli 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu amenewa ndidzawalanga kwambiri ndi kuwadzudzula mwaukali,+ ndipo ndikadzawalanga adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+
5 Pamenepo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzatambasula dzanja langa ndi kukantha Iguputo.+ Motero ndidzatulutsa ana a Isiraeli m’dzikolo.”+
22 Pa tsiku limenelo ndidzapatula dera la Goseni kumene kuli anthu anga, kuti kusakhale tizilombo toyamwa magazi.+ Ndidzatero kuti udziwe kuti ine ndine Yehova, ndipo ndili ndi mphamvu padziko lonse lapansi.+
17 Anthu amenewa ndidzawalanga kwambiri ndi kuwadzudzula mwaukali,+ ndipo ndikadzawalanga adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+