Ekisodo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Mose ndi Aroni anachitadi monga momwe Yehova anawalamulira.+ Anachitadi momwemo.+ Ekisodo 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo ana a Isiraeli anachoka ndi kukachita monga momwe Yehova analamulira Mose ndi Aroni.+ Anachitadi momwemo.
28 Pamenepo ana a Isiraeli anachoka ndi kukachita monga momwe Yehova analamulira Mose ndi Aroni.+ Anachitadi momwemo.