Genesis 46:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu anapitiriza kuti: “Ine ndine Mulungu woona,+ Mulungu wa bambo ako.+ Usaope kupita ku Iguputo, chifukwa kumeneko ndidzakukuza kukhala mtundu waukulu.+ Genesis 47:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Aisiraeliwo anakhazikika m’dziko la Iguputo, m’chigawo cha Goseni.+ Kumeneko anaberekana n’kuchulukana kwambiri.+ Machitidwe 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mulungu wa anthu awa Aisiraeli, anasankha makolo athu akale. Anakweza anthu amenewa pamene anali kukhala m’dziko lachilendo la Iguputo, ndipo anawatulutsa mmenemo ndi dzanja lokwezeka.+
3 Mulungu anapitiriza kuti: “Ine ndine Mulungu woona,+ Mulungu wa bambo ako.+ Usaope kupita ku Iguputo, chifukwa kumeneko ndidzakukuza kukhala mtundu waukulu.+
27 Aisiraeliwo anakhazikika m’dziko la Iguputo, m’chigawo cha Goseni.+ Kumeneko anaberekana n’kuchulukana kwambiri.+
17 Mulungu wa anthu awa Aisiraeli, anasankha makolo athu akale. Anakweza anthu amenewa pamene anali kukhala m’dziko lachilendo la Iguputo, ndipo anawatulutsa mmenemo ndi dzanja lokwezeka.+