Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Ndipatulireni mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa ana a Isiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+

  • Ekisodo 13:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 pamenepo muzidzapereka kwa Yehova mwana aliyense woyamba kubadwa,+ ndi mwana aliyense wa ziweto zanu woyamba kubadwa.+ Chachimuna chilichonse n’cha Yehova.+

  • Deuteronomo 21:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pakuti ayenera kuvomereza kuti mwana wamwamuna wa mkazi wake wosakondedwayo ndiye woyamba kubadwa. Azivomereza mwa kum’patsa magawo awiri pa chilichonse chimene ali nacho,+ chifukwa mwanayo ndiye chiyambi cha mphamvu zake zobereka.+ Mwana ameneyo ndiye woyenera kulandira udindo wa mwana woyamba kubadwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena