Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 22:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “Popereka zokolola zako zambirizo komanso zotuluka moponderamo mphesa ndi moyengeramo mafuta zochulukazo, usapereke monyinyirika.+ Mwana wako wamwamuna woyamba kubadwa uzim’pereka kwa ine.+

  • Ekisodo 34:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Mwana aliyense woyamba kubadwa ndi wanga,+ ngakhalenso mwana woyamba kubadwa wa ziweto zanu zonse, ng’ombe ndi nkhosa.+

  • Numeri 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mwana woyamba kubadwa aliyense pakati pa ana a Isiraeli ndi wanga, kaya akhale wa munthu kapena wa nyama.+ Pa tsiku limene ndinapha mwana woyamba kubadwa aliyense m’dziko la Iguputo+ ndinawapatula kuti akhale anga.+

  • Deuteronomo 15:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Mwana aliyense wamphongo woyamba kubadwa wa ng’ombe kapena wa nkhosa uzim’patulira Yehova Mulungu wako.+ Usagwiritse ntchito mwana woyamba kubadwa wa ng’ombe, kapena kumeta ubweya wa mwana woyamba kubadwa wa nkhosa.+

  • Luka 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Izi zinali zogwirizana ndi zimene Malemba amanena m’chilamulo cha Yehova kuti: “Mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa adzakhala woyera kwa Yehova.”*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena