Numeri 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Sindingathe kuwasamalira ndekha anthuwa, chifukwa iwo ndi chimtolo chimene sindingathe kuchisenza.+ Deuteronomo 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Pa nthawi imeneyo ndinakuuzani kuti, ‘Ndekha sindikwanitsa kusenza mtolo wokutsogolerani.+ Machitidwe 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero atumwi 12 aja anaitana khamu la ophunzira ndi kunena kuti: “N’kosayenera kuti ife tisiye ntchito yophunzitsa mawu a Mulungu n’kuyamba kugawa chakudya.+
14 Sindingathe kuwasamalira ndekha anthuwa, chifukwa iwo ndi chimtolo chimene sindingathe kuchisenza.+
2 Chotero atumwi 12 aja anaitana khamu la ophunzira ndi kunena kuti: “N’kosayenera kuti ife tisiye ntchito yophunzitsa mawu a Mulungu n’kuyamba kugawa chakudya.+