Ekisodo 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithu mutopa nazo zimenezi, iwe ndi anthu amene uli nawowa, chifukwa ntchito imeneyi yakukulira kwambiri.+ Sungathe kuichita wekha.+ Deuteronomo 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Pa nthawi imeneyo ndinakuuzani kuti, ‘Ndekha sindikwanitsa kusenza mtolo wokutsogolerani.+
18 Ndithu mutopa nazo zimenezi, iwe ndi anthu amene uli nawowa, chifukwa ntchito imeneyi yakukulira kwambiri.+ Sungathe kuichita wekha.+