Genesis 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma m’badwo wachinayi udzabwerera kuno,+ chifukwa nthawi yoti Aamori alangidwe sinakwane.”+ Deuteronomo 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamene Wam’mwambamwamba anapereka cholowa kwa mitundu,+Pamene analekanitsa ana a Adamu,+Anaika malire a anthu+Poganizira chiwerengero cha ana a Isiraeli.+ Salimo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka ndi yake pamodzi ndi onse okhala panthakapo.+
8 Pamene Wam’mwambamwamba anapereka cholowa kwa mitundu,+Pamene analekanitsa ana a Adamu,+Anaika malire a anthu+Poganizira chiwerengero cha ana a Isiraeli.+
24 Dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka ndi yake pamodzi ndi onse okhala panthakapo.+