Levitiko 27:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Amenewa ndiwo malamulo+ amene Yehova anapatsa Mose paphiri la Sinai+ kuti apereke kwa ana a Isiraeli. Yohane 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Popeza Chilamulo chinaperekedwa kudzera mwa Mose,+ kukoma mtima kwakukulu+ komanso choonadi+ zinakhalako kudzera mwa Yesu Khristu.
34 Amenewa ndiwo malamulo+ amene Yehova anapatsa Mose paphiri la Sinai+ kuti apereke kwa ana a Isiraeli.
17 Popeza Chilamulo chinaperekedwa kudzera mwa Mose,+ kukoma mtima kwakukulu+ komanso choonadi+ zinakhalako kudzera mwa Yesu Khristu.