Ekisodo 28:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “Upangenso kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide woyenga bwino, ndipo ulembepo mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo, mawu akuti, ‘Chiyero n’cha Yehova.’+ Ekisodo 39:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero anapanga kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide woyenga bwino, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka. Analembapo mawu akuti: “Chiyero n’cha Yehova.”+ Mawuwa anawalemba mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo.
36 “Upangenso kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide woyenga bwino, ndipo ulembepo mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo, mawu akuti, ‘Chiyero n’cha Yehova.’+
30 Atatero anapanga kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide woyenga bwino, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka. Analembapo mawu akuti: “Chiyero n’cha Yehova.”+ Mawuwa anawalemba mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo.