Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 39:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Atatero anapanga kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide woyenga bwino, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka. Analembapo mawu akuti: “Chiyero n’cha Yehova.”+ Mawuwa anawalemba mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo.

  • Levitiko 8:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Anamuvekanso nduwira+ pamutu pake, n’kuika patsogolo pa nduwirayo kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.

  • 1 Mbiri 16:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 M’patseni Yehova ulemerero wa dzina lake,+

      Tengani mphatso n’kubwera nayo pamaso pake.+

      Gwadirani Yehova mutavala zovala zokongola ndi zopatulika.+

  • Salimo 93:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Zikumbutso zanu ndi zodalirika zedi.+

      Chiyero ndi choyenera nyumba yanu+ mpaka muyaya, inu Yehova.+

  • Zekariya 14:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Pa tsiku limenelo, pamabelu a mahatchi padzalembedwa mawu+ akuti ‘Chiyero n’cha Yehova!’+ Ndipo miphika yakukamwa kwakukulu+ ya m’nyumba ya Yehova adzaigwiritsa ntchito ngati mbale zolowa+ za paguwa lansembe.+

  • Aheberi 7:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pakuti mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndiyedi wotiyenerera.+ Iye ndi wokhulupirika,+ wosalakwa,+ wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa,+ ndipo wakwera pamwamba kwambiri kuposa kumwamba.+

  • 1 Petulo 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 chifukwa Malemba amati: “Mukhale oyera, chifukwa ine ndine woyera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena