Salimo 69:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti kudzipereka kwambiri panyumba yanu kwandidya,+Ndipo mnyozo wa anthu amene akukutonzani wagwa pa ine.+ Yesaya 53:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+ Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+ Chilango chotibweretsera mtendere chinam’gwera iyeyo,+ ndipo chifukwa cha zilonda zake+ ifeyo tachiritsidwa.+ Aefeso 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inde, tonsefe pa nthawi inayake pamene tinali pakati pawo, tinali kukhala motsatira zilakolako za thupi lathu.+ Tinali kuchita zofuna za thupi+ ndi maganizo, ndipo mwachibadwa tinali ana oyenera kulandira mkwiyo wa Mulungu,+ mofanana ndi ena onse.
9 Pakuti kudzipereka kwambiri panyumba yanu kwandidya,+Ndipo mnyozo wa anthu amene akukutonzani wagwa pa ine.+
5 Iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+ Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+ Chilango chotibweretsera mtendere chinam’gwera iyeyo,+ ndipo chifukwa cha zilonda zake+ ifeyo tachiritsidwa.+
3 Inde, tonsefe pa nthawi inayake pamene tinali pakati pawo, tinali kukhala motsatira zilakolako za thupi lathu.+ Tinali kuchita zofuna za thupi+ ndi maganizo, ndipo mwachibadwa tinali ana oyenera kulandira mkwiyo wa Mulungu,+ mofanana ndi ena onse.