Numeri 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Kunena za ana a Levi, iwo ndawapatsa chakhumi+ chilichonse mu Isiraeli monga cholowa chawo chifukwa cha utumiki wawo umene akuchita, utumiki wa pachihema chokumanako. Deuteronomo 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Samala kuti usataye Mlevi+ masiku onse amene udzakhala m’dzikolo.
21 “Kunena za ana a Levi, iwo ndawapatsa chakhumi+ chilichonse mu Isiraeli monga cholowa chawo chifukwa cha utumiki wawo umene akuchita, utumiki wa pachihema chokumanako.