Ekisodo 12:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Lamulo lililonse ligwire ntchito mofanana kwa mbadwa ndi kwa mlendo wokhala pakati panu.”+ Levitiko 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “‘Chigamulo chilichonse chigwire ntchito mofanana pakati panu, kwa mlendo wokhala pakati panu ndi kwa nzika,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+ Numeri 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu amene mwapanga mpingo limodzi ndi alendo amene akukhala pakati panu, mukhale ndi malamulo amodzi.+ Amenewa ndiwo malamulo amene inuyo muziwatsatira mpaka kalekale m’mibadwo yanu. Mlendo azikhala chimodzimodzi ndi inu pamaso pa Yehova.+
22 “‘Chigamulo chilichonse chigwire ntchito mofanana pakati panu, kwa mlendo wokhala pakati panu ndi kwa nzika,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+
15 Inu amene mwapanga mpingo limodzi ndi alendo amene akukhala pakati panu, mukhale ndi malamulo amodzi.+ Amenewa ndiwo malamulo amene inuyo muziwatsatira mpaka kalekale m’mibadwo yanu. Mlendo azikhala chimodzimodzi ndi inu pamaso pa Yehova.+