Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 13:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Iwo anabwera kwa Mose ndi Aroni, ndiponso kwa khamu lonse la ana a Isiraeli m’chipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera onsewo za ulendo wawo n’kuwaonetsa zipatso za kudzikolo.

  • Numeri 20:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kenako khamu lonse la ana a Isiraeli linanyamuka ku Kadesi+ kuja n’kukafika kuphiri la Hora.+

  • Deuteronomo 1:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Chotero munakhala ku Kadesi masiku ambiri.+

  • Deuteronomo 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndipo masiku amene tinayenda kuchokera ku Kadesi-barinea mpaka kuwoloka chigwa cha Zeredi anali zaka 38, kufikira m’badwo wa amuna otha kupita kunkhondo utatha pakati panu, monga mmene Yehova analumbirira kwa iwo.+

  • Oweruza 11:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Chifukwa Aisiraeli atatuluka mu Iguputo anayenda kudutsa m’chipululu kukafika ku Nyanja Yofiira+ mpaka ku Kadesi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena